Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mudzathamangitsa adani anu+ ndi kuwagonjetsa ndi lupanga.

  • Deuteronomo 32:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,

      Kapena anthu awiri angapitikitse bwanji anthu 10,000?+

      N’zosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+

      Komanso ngati Yehova atawapereka.

  • Yoswa 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atafika pamalo otsetsereka otchedwa Beti-horoni pothawa Aisiraeli, Yehova anawagwetsera miyala ikuluikulu ya matalala+ kuchokera kumwamba yomwe inawagwera ndi kuwapha mpaka kukafika ku Azeka. Amene anaphedwa ndi matalalawo anali ambiri kuposa amene ana a Isiraeli anapha ndi lupanga.

  • 2 Samueli 22:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Ndidzathamangitsa adani anga kuti ndiwafafanize,

      Ndipo sindidzabwerera kufikira nditawawononga onse.+

  • Salimo 89:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndinaphwanya adani ake zidutswazidutswa ndi kuwachotsa pamaso pake,+

      Ndipo odana naye kwambiri ndinapitirizabe kuwamenya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena