Yobu 38:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi unalowapo munkhokwe ya chipale chofewa,+Kapena umaziona nkhokwe za matalala,+ Salimo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto. Salimo 148:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+ Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+ Mabuku a Chichewa (1974-2025) Tulukani Lowani Chichewa Tumizirani Ena Zimene Mumakonda Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Zoyenera Kutsatira Nkhani Yosunga Chinsinsi Privacy Settings JW.ORG Lowani Tumizirani Ena Tumizirani Wina pa Imelo
22 Kodi unalowapo munkhokwe ya chipale chofewa,+Kapena umaziona nkhokwe za matalala,+ Salimo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto. Salimo 148:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+ Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto.
8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+ Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+