Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo.

  • Numeri 16:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ndiyeno panabuka moto wochokera kwa Yehova,+ umene unapsereza amuna 250 omwe anali kupereka nsembe zofukiza+ aja.

  • Salimo 147:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Amaponya madzi oundana ngati nyenyeswa za chakudya.+

      Ndani angaime m’chisanu chake?+

  • Yesaya 30:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena