-
Numeri 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Aliyense akatenge chofukizira chake. Mukaikemo nsembe yofukiza, ndipo aliyense adzabweretse chofukizira chake pamaso pa Yehova. Zofukizirazo zidzakhalepo zokwanira 250, komanso iweyo ndi Aroni aliyense adzakhale ndi chake.”
-