Salimo 148:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+ Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
8 Inu moto ndi matalala, chipale chofewa ndi utsi wakuda bii,+Iwe mphepo yamkuntho yokwaniritsa mawu ake.+ Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+