Oweruza 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Gidiyoni atangomva lotolo ndi tanthauzo lake,+ analambira Mulungu.+ Kenako anabwerera kumsasa wa Isiraeli ndi kuwauza kuti: “Tiyeni,+ pakuti Yehova wapereka msasa wa Amidiyani m’manja mwanu.” Yeremiya 48:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wotembereredwa ndi munthu wozengereza kugwira ntchito imene Yehova wamupatsa.+ Wotembereredwa ndi munthu wopewa kukhetsa magazi ndi lupanga lake.
15 Gidiyoni atangomva lotolo ndi tanthauzo lake,+ analambira Mulungu.+ Kenako anabwerera kumsasa wa Isiraeli ndi kuwauza kuti: “Tiyeni,+ pakuti Yehova wapereka msasa wa Amidiyani m’manja mwanu.”
10 “Wotembereredwa ndi munthu wozengereza kugwira ntchito imene Yehova wamupatsa.+ Wotembereredwa ndi munthu wopewa kukhetsa magazi ndi lupanga lake.