Ekisodo 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+ 2 Mbiri 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi yomweyo Yehosafati anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo Ayuda onse ndi anthu okhala mu Yerusalemu anawerama pamaso pa Yehova kuti alambire Yehovayo.+ Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+
31 Zitatero anthuwo anakhulupirira+ Mose. Atamva kuti Yehova wacheukira+ ana a Isiraeli, ndi kutinso waona nsautso yawo,+ anagwada ndi kuweramira pansi.+
18 Nthawi yomweyo Yehosafati anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo Ayuda onse ndi anthu okhala mu Yerusalemu anawerama pamaso pa Yehova kuti alambire Yehovayo.+