Numeri 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo iye anawafunsa kuti: “Kodi akazi onse mwawasiya amoyo?+ Oweruza 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mngelo wa Yehova+ anati: ‘Tembererani+ Merozi,Tembererani anthu ake mosaleka,Chifukwa sanathandize Yehova,Sanabwere ndi anthu amphamvu kudzathandiza Yehova.’ 1 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye n’chifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira zofunkha mosusuka+ ndi kuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”+ 1 Mafumu 20:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+
23 Mngelo wa Yehova+ anati: ‘Tembererani+ Merozi,Tembererani anthu ake mosaleka,Chifukwa sanathandize Yehova,Sanabwere ndi anthu amphamvu kudzathandiza Yehova.’
19 Ndiye n’chifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira zofunkha mosusuka+ ndi kuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”+
42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+