Ekisodo 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti mngelo wanga adzakutsogolera ndi kukulowetsa m’dziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi, ndipo ndidzawafafaniza ndithu.+ Oweruza 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu,+ ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo ndi kukulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Komanso ndinakuuzani kuti, ‘Sindidzaphwanya konse pangano langa ndi inu.+
23 Pakuti mngelo wanga adzakutsogolera ndi kukulowetsa m’dziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi, ndipo ndidzawafafaniza ndithu.+
2 Ndiyeno mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu,+ ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo ndi kukulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Komanso ndinakuuzani kuti, ‘Sindidzaphwanya konse pangano langa ndi inu.+