21 Yehova adzaimirira monga mmene anachitira paphiri la Perazimu.+ Adzakalipa ngati mmene anachitira m’chigwa cha kufupi ndi Gibeoni+ kuti achite ntchito yake. Ntchito yakeyo ndi yodabwitsa. Adzakalipa kuti achite zochita zake. Zochita zakezo n’zachilendo.+