Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+

  • Yeremiya 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iwe unali kuvala zovala zamtengo wapatali,* unali kudzikongoletsa ndi zokongoletsera zagolide ndipo unali kudzikongoletsa m’maso mwako ndi utoto wakuda.+ Tsopano utani popeza wafunkhidwa? Unali kutaya nthawi ndi kudzikongoletsa.+ Amene anali kukukhumba tsopano akukukana ndipo akufunafuna moyo wako.+

  • Ezekieli 23:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Adzakuvula zovala zako+ ndi kutenga zinthu zako zokongola.+

  • Hoseya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 kuti ndisamuvule ndi kumukhalitsa wamaliseche+ ngati tsiku limene anabadwa,+ kutinso ndisamuchititse kukhala ngati chipululu+ ndi dziko lopanda madzi+ ndiponso kuti ndisamuphe ndi ludzu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena