Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 13:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka.

  • Ezekieli 16:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndidzakupereka m’manja mwa anthu okuukira ndipo iwo adzafafaniza mulu wako wadothi+ ndi malo ako okwera.+ Iwo adzakuvula zovala+ ndipo adzatenga zinthu zako zokongola+ n’kukusiya wosavala ndi wamaliseche.

  • Hoseya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 kuti ndisamuvule ndi kumukhalitsa wamaliseche+ ngati tsiku limene anabadwa,+ kutinso ndisamuchititse kukhala ngati chipululu+ ndi dziko lopanda madzi+ ndiponso kuti ndisamuphe ndi ludzu.+

  • Chivumbulutso 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nyanga 10+ waziona zija, komanso chilombo,+ zimenezi zidzadana nalo hulelo.+ Zidzalisakaza ndi kulisiya lamaliseche. Zidzadya minofu yake ndi kulinyeketsa ndi moto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena