Chivumbulutso 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mngelo uja anandifunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukudabwa? Ndikuuza chinsinsi cha mkazi ameneyu,+ ndi cha chilombo chimene wakwerapo, chokhala ndi mitu 7 ndi nyanga 10:+
7 Koma mngelo uja anandifunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukudabwa? Ndikuuza chinsinsi cha mkazi ameneyu,+ ndi cha chilombo chimene wakwerapo, chokhala ndi mitu 7 ndi nyanga 10:+