Chivumbulutso 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mu mphamvu ya mzimu,+ mngeloyo ananditengera kuchipululu. Ndipo ndinaona mkazi atakhala pachilombo+ chofiira kwambiri, chodzaza ndi mayina onyoza Mulungu.+ Chinali ndi mitu 7,+ ndi nyanga 10.
3 Mu mphamvu ya mzimu,+ mngeloyo ananditengera kuchipululu. Ndipo ndinaona mkazi atakhala pachilombo+ chofiira kwambiri, chodzaza ndi mayina onyoza Mulungu.+ Chinali ndi mitu 7,+ ndi nyanga 10.