Ezekieli 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Dzanja la Yehova linali pa ine+ moti mzimu wa Yehova unanditenga+ ndi kukandikhazika m’chigwa mmene munali mafupa okhaokha.+ Chivumbulutso 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa mzimu,+ ndinapezeka kuti ndili+ m’tsiku la Ambuye,+ ndipo kumbuyo kwanga ndinamva mawu amphamvu+ ngati kulira kwa lipenga.
37 Dzanja la Yehova linali pa ine+ moti mzimu wa Yehova unanditenga+ ndi kukandikhazika m’chigwa mmene munali mafupa okhaokha.+
10 Mwa mzimu,+ ndinapezeka kuti ndili+ m’tsiku la Ambuye,+ ndipo kumbuyo kwanga ndinamva mawu amphamvu+ ngati kulira kwa lipenga.