Danieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+ Chivumbulutso 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10+ amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi.
24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+
12 “Nyanga 10 zimene unaona zija, zikuimira mafumu 10+ amene sanalandirebe ufumu wawo. Koma adzalandira ulamuliro monga mafumu ndipo adzalamulira limodzi ndi chilombo kwa ola limodzi.