Genesis 38:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+ Levitiko 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+ Chivumbulutso 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+
24 Patapita miyezi itatu, Yuda anauzidwa kuti: “Tamara mpongozi wako anachita chiwerewere,+ ndipo ali ndi pakati.”+ Yuda atamva zimenezo, anati: “M’tulutseni kuti aphedwe ndi kuotchedwa.”+
9 “‘Mwana wamkazi wa wansembe akadziipitsa mwa kuchita uhule, pamenepo waipitsa bambo ake. Aziphedwa ndi kutenthedwa.+
8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+