Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 momwemonso mfumu ya Asuri idzagwira gulu la anthu ku Iguputo+ ndi ku Itiyopiya n’kupita nawo ku ukapolo kudziko lina, anyamata ndi nkhalamba, ali opanda zovala ndi opanda nsapato, ndiponso matako awo ali pamtunda. Pamenepo, umaliseche wa Iguputo udzaonekera.+

  • Ezekieli 16:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+

  • Hoseya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 kuti ndisamuvule ndi kumukhalitsa wamaliseche+ ngati tsiku limene anabadwa,+ kutinso ndisamuchititse kukhala ngati chipululu+ ndi dziko lopanda madzi+ ndiponso kuti ndisamuphe ndi ludzu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena