Yesaya 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapereka Iguputo m’manja mwa mbuye wankhanza ndipo mfumu imene idzawalamulire idzakhala yamphamvu,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa makamu. Yeremiya 46:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Ndidzapereka anthu a ku Iguputo m’manja mwa anthu amene akufuna moyo wawo, m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ ndi m’manja mwa atumiki ake. Kenako anthu adzakhalanso m’dzikolo monga mmene zinalili kale,’+ watero Yehova. Ezekieli 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzapereka ziweruzo mu Iguputo+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
4 Ndidzapereka Iguputo m’manja mwa mbuye wankhanza ndipo mfumu imene idzawalamulire idzakhala yamphamvu,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa makamu.
26 “‘Ndidzapereka anthu a ku Iguputo m’manja mwa anthu amene akufuna moyo wawo, m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ ndi m’manja mwa atumiki ake. Kenako anthu adzakhalanso m’dzikolo monga mmene zinalili kale,’+ watero Yehova.