Yeremiya 46:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Ndidzapereka anthu a ku Iguputo mʼmanja mwa anthu amene akufuna moyo wawo, mʼmanja mwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo+ ndi mʼmanja mwa atumiki ake. Koma kenako anthu adzakhalanso mʼdzikolo ngati mmene zinalili kale,’ akutero Yehova.+
26 ‘Ndidzapereka anthu a ku Iguputo mʼmanja mwa anthu amene akufuna moyo wawo, mʼmanja mwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo+ ndi mʼmanja mwa atumiki ake. Koma kenako anthu adzakhalanso mʼdzikolo ngati mmene zinalili kale,’ akutero Yehova.+