-
Ezekieli 29:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Zaka 40 zikadzatha, ndidzasonkhanitsanso Aiguputowo nʼkuwabwezera kudziko lawo kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anabalalikira.+ 14 Aiguputo amene anagwidwa nʼkupita nawo kudziko lina ndidzawabwezeretsa ku Patirosi,+ mʼdziko limene anachokera ndipo kumeneko Iguputo adzakhala ufumu wonyozeka.
-