Yesaya 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapereka Iguputo mʼmanja mwa mbuye wankhanzaNdipo mfumu yankhanza idzawalamulira,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:4 Yesaya 1, ptsa. 200-202 Nsanja ya Olonda,2/1/1988, tsa. 27
4 Ndidzapereka Iguputo mʼmanja mwa mbuye wankhanzaNdipo mfumu yankhanza idzawalamulira,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.