Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 9:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kenako Yehu anafika ku Yezereeli,+ ndipo Yezebeli+ anamva zimenezo. Yezebeliyo anadzikongoletsa podzipaka utoto+ wakuda m’maso mwake n’kukongoletsanso tsitsi lake mochititsa kaso.+ Atatero anakaima pawindo n’kumayang’ana kunja.+

  • Ezekieli 23:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Kuwonjezera apo, akaziwo atatumiza uthenga kwa amuna ochokera kutali, amuna amene anawatumizira uthengawo+ anabweradi.+ Iwe unasamba,+ n’kupaka zodzikongoletsera m’maso,+ ndi kuvala zodzikongoletsera kuti amuna amenewa akuone.+

  • Chivumbulutso 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mkaziyo anavala zovala zofiirira+ ndi zofiira kwambiri.+ Anadzikongoletsa ndi golide, ndi mwala winawake wamtengo wapatali, ndiponso ngale.+ M’dzanja lake, anali ndi kapu yagolide+ yodzaza ndi zonyansa+ ndi zinthu zodetsedwa zokhudzana ndi dama lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena