Yesaya 57:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe unatsetserekera kwa Meleki utatenga mafuta, ndipo unachulukitsa mafuta ako onunkhira.+ Unapitiriza kutumiza nthumwi zako kutali kwambiri moti mpaka unatsitsira zochita zako m’Manda.+
9 Iwe unatsetserekera kwa Meleki utatenga mafuta, ndipo unachulukitsa mafuta ako onunkhira.+ Unapitiriza kutumiza nthumwi zako kutali kwambiri moti mpaka unatsitsira zochita zako m’Manda.+