Salimo 55:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chiwonongeko chiwagwere!+Atsikire ku Manda ali amoyo.+Pakuti kulikonse kumene apita, zinthu zoipa zimakhala mumtima mwawo.+ Miyambo 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nyumba yake ndiyo njira ya ku Manda.+ Imatsikira kuzipinda za imfa.+
15 Chiwonongeko chiwagwere!+Atsikire ku Manda ali amoyo.+Pakuti kulikonse kumene apita, zinthu zoipa zimakhala mumtima mwawo.+