Miyambo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti nyumba yake imatsikira kumanda ndipo njira zake zimatsikira kwa akufa.+ Mlaliki 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usakhale woipa mopitirira muyezo,+ komanso usakhale wopusa.+ Uferenji mwamsanga?+