Miyambo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapazi ake amatsikira ku imfa.+ Miyendo yake imalowera ku Manda.+ Miyambo 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye adzafa chifukwa chosamvera malangizo,+ ndiponso chifukwa chakuti amasocheretsedwa ndi zopusa zake zochuluka.+ Miyambo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma mwamunayo sakudziwa kuti kumeneko kuli akufa, ndiponso kuti amene amaitanidwa ndi mkaziyu ali kumalo otsika a ku Manda.+ Aefeso 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+
23 Iye adzafa chifukwa chosamvera malangizo,+ ndiponso chifukwa chakuti amasocheretsedwa ndi zopusa zake zochuluka.+
18 Koma mwamunayo sakudziwa kuti kumeneko kuli akufa, ndiponso kuti amene amaitanidwa ndi mkaziyu ali kumalo otsika a ku Manda.+
5 Pakuti mfundo iyi mukuidziwa, ndipo mukuimvetsa bwino, kuti wadama+ kapena wodetsedwa kapena waumbombo,+ umene ndiwo kupembedza mafano, sadzalowa mu ufumu wa Khristu ndi wa Mulungu.+