Miyambo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amene wagwira malangizo* mwamphamvu ndiye njira ya kumoyo,+ koma wosiya chidzudzulo amasocheretsa anthu.+
17 Amene wagwira malangizo* mwamphamvu ndiye njira ya kumoyo,+ koma wosiya chidzudzulo amasocheretsa anthu.+