Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndinaona mkazi akubwera kudzakumana naye atavala zovala zosonyeza kuti ndi hule.+ Mkaziyo anali wamtima wachinyengo,

  • Yesaya 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 M’tsiku limenelo Yehova adzachotsa zokongoletsera zawo zonse: zibangili za m’miyendo, zinthu zomanga kumutu, zodzikongoletsera zooneka ngati mwezi,+

  • Ezekieli 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Unali kuvala zinthu zagolide ndi zasiliva ndiponso nsalu zabwino kwambiri. Unali kuvala nsalu zamtengo wapatali ndi chovala cha nsalu yopeta.+ Unkadya ufa wosalala, uchi, ndi mafuta+ ndipo unakhala chiphadzuwa. Patapita nthawi unakhala woyenera ufumu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena