Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 22:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Pita ku Lebanoni+ kuti ukalire kumeneko, ndipo ukafuule ku Basana.+ Ukalirenso ku Abarimu+ chifukwa amene anali kukukonda kwambiri agonjetsedwa.+

  • Maliro 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+

      Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+

      Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+

  • Chivumbulutso 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nyanga 10+ waziona zija, komanso chilombo,+ zimenezi zidzadana nalo hulelo.+ Zidzalisakaza ndi kulisiya lamaliseche. Zidzadya minofu yake ndi kulinyeketsa ndi moto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena