Salimo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”“Ndi Yehova wa makamu. Iye ndiye Mfumu yaulemerero.”+ [Seʹlah.] Salimo 74:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+
10 “Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndani?”“Ndi Yehova wa makamu. Iye ndiye Mfumu yaulemerero.”+ [Seʹlah.]
12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,+Iye ndiye wondipatsa chipulumutso chachikulu padziko lapansi.+
22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+