Mateyu 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.” Aheberi 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+
24 Poona kuti sizikuthandiza, komanso pakuyambika chipolowe, Pilato anangotenga madzi+ ndi kusamba m’manja pamaso pa khamu la anthulo, n’kunena kuti: “Inetu ndasamba m’manja, ndilibe mlandu wa magazi a munthu uyu. Zonse zili kwa inu.”
26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+