10 Lero mwadzionera nokha kuti Yehova anakuperekani m’manja mwanga m’phangamu. Winawake anandiuza kuti ndikupheni,+ koma ndinakumverani chisoni n’kunena kuti, ‘Sindingatambasule dzanja langa ndi kuukira mbuyanga, pakuti iye ndi wodzozedwa+ wa Yehova.’