-
1 Samueli 24:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Amuna amene anali ndi Davidewo anayamba kumuuza kuti: “Lerotu ndi tsiku limene Yehova akukuuzani kuti, ‘Taona, ndapereka mdani wako m’manja mwako,+ ndipo umuchitire chilichonse chimene ukuona kuti n’chabwino.’”+ Choncho Davide ananyamuka ndipo mwakachetechete anadula kansalu m’munsi mwa malaya akunja odula manja a Sauli.
-