1 Samueli 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wako m’manja mwako.+ Ndiye ndilole chonde, ndimubaye ndi kumukhomerera pansi ndi mkondo kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.” 1 Samueli 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova adzabwezera aliyense malinga ndi chilungamo+ ndi kukhulupirika kwake, pakuti lero Yehova anakuperekani m’manja mwanga, koma sindinafune kutambasula dzanja langa ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+
8 Tsopano Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wako m’manja mwako.+ Ndiye ndilole chonde, ndimubaye ndi kumukhomerera pansi ndi mkondo kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.”
23 Yehova adzabwezera aliyense malinga ndi chilungamo+ ndi kukhulupirika kwake, pakuti lero Yehova anakuperekani m’manja mwanga, koma sindinafune kutambasula dzanja langa ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+