1 Mafumu 8:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+ Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+ Salimo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+ Salimo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muwabwezere mogwirizana ndi zochita zawo,+Mogwirizana ndi kuipa kwa zochita zawo.+Abwezereni mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+Abwezereni zochita zawo.+
32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera mogwirizana ndi njira yake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+
20 Yehova amandipatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo changa.+Amandibwezera mogwirizana ndi kuyera kwa manja anga.+
4 Muwabwezere mogwirizana ndi zochita zawo,+Mogwirizana ndi kuipa kwa zochita zawo.+Abwezereni mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+Abwezereni zochita zawo.+