Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho iye anauza amuna amene anali kuyenda naye kuti: “Sindinayenere m’pang’ono pomwe kuchitira mbuyanga zimenezi pamaso pa Yehova. Iye ndi wodzozedwa+ wa Yehova. Sindinayenere kutambasula dzanja langa ndi kumuukira, pakuti iye ndi wodzozedwa wa Yehova.”+

  • 1 Samueli 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma Davide anauza Abisai kuti: “Ayi, usamuphe. Kodi ndani anatambasula dzanja lake ndi kupha wodzozedwa wa Yehova,+ n’kukhala wopanda mlandu?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena