1 Petulo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi, ndani angakuchitireni zoipa mukakhala odzipereka pochita zabwino?+ 1 Yohane 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+
12 osati ngati Kaini, amene anachokera kwa woipayo n’kupha+ m’bale wake. N’chifukwa chiyani iye anapha m’bale wake? Chifukwa chakuti zochita zake zinali zoipa,+ koma za m’bale wake zinali zolungama.+