Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+

      Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+

      Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+

      Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+

  • Deuteronomo 32:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+

      Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+

      Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+

      Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”

  • Yeremiya 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Kodi sindiyenera kuwalanga chifukwa cha zinthu zimenezi?” watero Yehova. “Kapena kodi sindiyenera kubwezera mtundu wa anthu amakhalidwe oterewa?+

  • Hoseya 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Masiku oti uyenderedwe adzafika,+ masiku oti ulipire adzakwana+ ndipo anthu a Isiraeli adzadziwa zimenezi.+ Mneneri adzapusa+ ndipo munthu wolankhula mawu ouziridwa adzalusa, chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zako+ ndiponso chifukwa cha kuchuluka kwa chidani.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena