1 Akorinto 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano sitinalandire mzimu+ wa dziko, koma mzimu+ wochokera kwa Mulungu, kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.+ 2 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye watiikanso chidindo+ chake chotitsimikizira ndipo watipatsa m’mitima mwathu chikole+ cha madalitso am’tsogolo, ndicho mzimu.+ 2 Timoteyo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Mulungu sanatipatse mzimu wamantha,+ koma wamphamvu,+ wachikondi, ndi woti tiziganiza bwino.+
12 Tsopano sitinalandire mzimu+ wa dziko, koma mzimu+ wochokera kwa Mulungu, kuti tidziwe zinthu zimene Mulungu watipatsa mokoma mtima.+
22 Iye watiikanso chidindo+ chake chotitsimikizira ndipo watipatsa m’mitima mwathu chikole+ cha madalitso am’tsogolo, ndicho mzimu.+
7 Pakuti Mulungu sanatipatse mzimu wamantha,+ koma wamphamvu,+ wachikondi, ndi woti tiziganiza bwino.+