1 Yohane 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mawu alionse ouziridwa amene amatsutsa zoti Yesu anabwera monga munthu, amenewo si ochokera kwa Mulungu,+ ndipo ndi ouziridwa ndi wokana Khristu amene munamva kuti akubwera,+ ndipo tsopano ali kale m’dziko.+ 1 Yohane 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tikudziwa kuti tinachokera kwa Mulungu,+ koma dziko lonse lili m’manja mwa woipayo.+ Chivumbulutso 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+
3 Koma mawu alionse ouziridwa amene amatsutsa zoti Yesu anabwera monga munthu, amenewo si ochokera kwa Mulungu,+ ndipo ndi ouziridwa ndi wokana Khristu amene munamva kuti akubwera,+ ndipo tsopano ali kale m’dziko.+
14 Kwenikweni amenewa ndi mauthenga ouziridwa+ ndi ziwanda ndipo amachita zizindikiro.+ Mauthengawo akupita kwa mafumu+ a dziko lonse lapansi+ kumene kuli anthu, kuti awasonkhanitsire pamodzi kunkhondo+ ya tsiku lalikulu+ la Mulungu Wamphamvuyonse.+