2 Atesalonika 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zoona, chinsinsi cha kusamvera malamulo kumeneku chilipo kale,+ koma chingokhalapo kufikira atachoka amene panopa ali choletsa.+ 1 Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto,+ ndipo monga mmene munamvera kuti wokana Khristu akubwera,+ ngakhale panopa alipo okana Khristu ambiri.+ Chifukwa cha zimenezi timadziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.
7 Zoona, chinsinsi cha kusamvera malamulo kumeneku chilipo kale,+ koma chingokhalapo kufikira atachoka amene panopa ali choletsa.+
18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto,+ ndipo monga mmene munamvera kuti wokana Khristu akubwera,+ ngakhale panopa alipo okana Khristu ambiri.+ Chifukwa cha zimenezi timadziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.