2 Atesalonika 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zoona, kuipa kwa munthu ameneyu, komwe ndi kwachinsinsi, kwayamba kale kugwira ntchito.+ Koma kuipa kumeneku kupitiriza kukhala chinsinsi mpaka amene akumulepheretsa atachoka. 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Utumiki Komanso Moyo Wathu,7/2019, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,2/1/1990, tsa. 101/15/1990, ptsa. 18-19
7 Zoona, kuipa kwa munthu ameneyu, komwe ndi kwachinsinsi, kwayamba kale kugwira ntchito.+ Koma kuipa kumeneku kupitiriza kukhala chinsinsi mpaka amene akumulepheretsa atachoka.
2:7 Utumiki Komanso Moyo Wathu,7/2019, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,2/1/1990, tsa. 101/15/1990, ptsa. 18-19