Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 20:29, 30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu yopondereza idzafika pakati panu+ ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+

  • 1 Akorinto 11:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choyamba, ndamva kuti mukasonkhana mumpingo, pakumakhala kugawanika, ndipo kumbali ina ndikuona kuti ndi zoona. 19 Payeneradi kukhala magulu ampatuko pakati panu,+ kuti anthu ovomerezeka kwa Mulungu adziwike.

  • 1 Yohane 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena