Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Atesalonika 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zoona, kuipa kwa munthu ameneyu, komwe ndi kwachinsinsi, kwayamba kale kugwira ntchito.+ Koma kuipa kumeneku kupitiriza kukhala chinsinsi mpaka amene akumulepheretsa atachoka.

  • 2 Yohane 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komabe samalani chifukwa anthu ambiri opusitsa anzawo ayamba kupezeka mʼdzikoli.+ Anthu amenewa amatsutsa zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wopusitsa ena ndiponso wokana Khristu.+

  • Yuda 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndatero chifukwa chakuti anthu ena alowa mozemba pakati panu. Malemba anasonyezeratu kalekale kuti anthu amenewa adzaweruzidwa. Anthuwa ndi osaopa Mulungu ndipo atenga kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu kukhala chifukwa chochitira khalidwe lopanda manyazi.*+ Komanso asonyeza kuti ndi osakhulupirika kwa Ambuye wathu mmodzi yekha amene anatigula, Yesu Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena