2 Timoteyo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ine ndayamba kale kukhuthulidwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndipo nthawi yakuti ndimasuke+ yatsala pang’ono kukwana. 2 Petulo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 popeza ndikudziwa kuti ndatsala pang’ono kutuluka mumsasa wangawu,+ monga momwe Ambuye wathu Yesu Khristu anandisonyezera.+
6 Pakuti ine ndayamba kale kukhuthulidwa ngati nsembe yachakumwa,+ ndipo nthawi yakuti ndimasuke+ yatsala pang’ono kukwana.
14 popeza ndikudziwa kuti ndatsala pang’ono kutuluka mumsasa wangawu,+ monga momwe Ambuye wathu Yesu Khristu anandisonyezera.+