Yohane 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+
18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+