1 Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:18 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,6/1/2015, tsa. 141/15/1987, tsa. 30 Kukambitsirana, tsa. 414
18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.
2:18 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,6/1/2015, tsa. 141/15/1987, tsa. 30 Kukambitsirana, tsa. 414