Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndiye kunabwera akapolo a mwinimunda uja kudzamuuza kuti, ‘Mbuye, kodi simunafese mbewu zabwino m’munda wanuwu?+ Nanga namsongoleyu wachokeranso kuti?’+

  • 2 Atesalonika 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zoona, chinsinsi cha kusamvera malamulo kumeneku chilipo kale,+ koma chingokhalapo kufikira atachoka amene panopa ali choletsa.+

  • 2 Yohane 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 popeza anthu onyenga ambiri alowa m’dziko,+ amene amatsutsa zakuti kalero Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wonyenga+ uja ndiponso wokana Khristu.+

  • Yuda 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndatero chifukwa chakuti anthu ena alowa mozemba pakati pathu.+ Anthu amenewa Malemba anawasonyezeratu kalekale+ kuti adzaweruzidwa.+ Iwo ndiwo anthu osaopa Mulungu+ amene atenga kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu wathu kukhala chifukwa chochitira khalidwe lotayirira,+ ndipo akhala osakhulupirika+ kwa Ambuye wathu mmodzi yekha+ amene anatigula,+ Yesu Khristu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena