Miyambo 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nsembe ya anthu oipa ndi yonyansa.+ Ndiye kuli bwanji munthu akaiperekera limodzi ndi makhalidwe otayirira?+ 2 Akorinto 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwina ndikadzabweranso, Mulungu wanga adzandichititsa manyazi pakati panu. Ndipo mwina ndidzalirira anthu ambiri amene anachimwa+ koma sanalape pa zonyansa zawo, dama*+ lawo, ndi khalidwe lawo lotayirira+ limene akhala akuchita. Agalatiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+ 2 Petulo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+
27 Nsembe ya anthu oipa ndi yonyansa.+ Ndiye kuli bwanji munthu akaiperekera limodzi ndi makhalidwe otayirira?+
21 Mwina ndikadzabweranso, Mulungu wanga adzandichititsa manyazi pakati panu. Ndipo mwina ndidzalirira anthu ambiri amene anachimwa+ koma sanalape pa zonyansa zawo, dama*+ lawo, ndi khalidwe lawo lotayirira+ limene akhala akuchita.
19 Tsopano, ntchito za thupi zimaonekera.+ Ntchitozi ndizo dama,*+ zinthu zodetsa, khalidwe lotayirira,+
14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+